fie.nipa,

Jollof

Jollof amandia chiyani?

Jollof amandia chakudya.

Ife timafunika ....

  • mpunga
  • tomato
  • tsabola
  • mchere
  • anyezi
  • nyama kapena nsomba
  • mafuta

<< Previous | Next >>