Nududu,

Mpunga - Waakye

Waakye ndi chchakudya chza mpunga.

Ife timakonda Waakye.

Ife timafunika ....

  • mpunga
  • nyemba
  • tomato
  • tsabola
  • mchere
  • anyezi
  • nyama kapena nsomba
  • mafuta
  • galimoto
<< [Adj:Previous] | Ijayo >>